2 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+
4 ndipo anapitiriza kutipempha mochokera pansi pa mtima ndiponso mochonderera kwambiri, kuti tiwapatse mwayi wopereka nawo mphatso zachifundo ndi kutinso achite nawo utumiki wothandiza oyerawo.+