Yesaya 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 M’tsiku limenelo, padzakhala msewu waukulu+ wochokera ku Iguputo kupita ku Asuri. Anthu a ku Asuri adzapita ku Iguputo ndipo anthu a ku Iguputo adzapita ku Asuri. Aiguputo ndi Asuri adzatumikira Mulungu limodzi.
23 M’tsiku limenelo, padzakhala msewu waukulu+ wochokera ku Iguputo kupita ku Asuri. Anthu a ku Asuri adzapita ku Iguputo ndipo anthu a ku Iguputo adzapita ku Asuri. Aiguputo ndi Asuri adzatumikira Mulungu limodzi.