Yesaya 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku limenelo, padzakhala msewu waukulu+ wochokera ku Iguputo kupita ku Asuri. Anthu a ku Asuri adzapita ku Iguputo ndipo anthu a ku Iguputo adzapita ku Asuri. Aiguputo adzatumikira Mulungu limodzi ndi Asuri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:23 Yesaya 1, ptsa. 206-207
23 Pa tsiku limenelo, padzakhala msewu waukulu+ wochokera ku Iguputo kupita ku Asuri. Anthu a ku Asuri adzapita ku Iguputo ndipo anthu a ku Iguputo adzapita ku Asuri. Aiguputo adzatumikira Mulungu limodzi ndi Asuri.