Yesaya 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 M’tsiku limenelo, padzakhala msewu waukulu+ wochokera ku Iguputo kupita ku Asuri. Anthu a ku Asuri adzapita ku Iguputo ndipo anthu a ku Iguputo adzapita ku Asuri. Aiguputo ndi Asuri adzatumikira Mulungu limodzi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:23 Yesaya 1, ptsa. 206-207
23 M’tsiku limenelo, padzakhala msewu waukulu+ wochokera ku Iguputo kupita ku Asuri. Anthu a ku Asuri adzapita ku Iguputo ndipo anthu a ku Iguputo adzapita ku Asuri. Aiguputo ndi Asuri adzatumikira Mulungu limodzi.