-
1 Mbiri 12:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kenako Amasai, mkulu wa asilikali 30, anayankha mothandizidwa ndi mzimu+ kuti:
“Ife ndife anthu anu, inu a Davide ndipo tili kumbali yanu inu mwana wa Jese.+
Mtendere ukhale nanu ndiponso mtendere ukhale ndi amene akukuthandizani,
Chifukwa Mulungu wanu akukuthandizani.”+
Choncho Davide anawalandira nʼkuwaika mʼgulu la atsogoleri a asilikali.
-