Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Usachite pangano ndi iwo kapena milungu yawo.+

  • Deuteronomo 7:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.

  • Deuteronomo 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 milungu ina mwa milungu ya anthu okuzungulirani, okhala pafupi nanu kapena okhala kutali, kuchokera kumalekezero ena a dziko kukafika kumalekezero ena,

  • Oweruza 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komanso ndinakuuzani kuti: “Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Musaope milungu ya Aamori+ amene mukukhala m’dziko lawo.”+ Koma inu simunamvere mawu anga.’”+

  • Oweruza 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zitatero, ana a Isiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ ndipo anayamba kutumikira Abaala,+ zifaniziro za Asitoreti,+ milungu ya ku Siriya,+ milungu ya ku Sidoni,+ milungu ya ku Mowabu,+ milungu ya ana a Amoni+ ndi milungu ya Afilisiti.+ Motero iwo anasiya Yehova ndipo sanam’tumikire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena