2 Mafumu 17:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 pamene Yehova anachita nawo pangano+ n’kuwalamula kuti: “Musamaope milungu ina.+ Musamaigwadire kapena kuitumikira kapenanso kupereka nsembe kwa iyo.+ Yeremiya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wanena kuti: “Musaphunzire njira za anthu a mitundu ina ngakhale pang’ono,+ ndipo musamaope zizindikiro zakumwamba, chifukwa anthu a mitundu ina amachita mantha ndi zizindikirozo.+
35 pamene Yehova anachita nawo pangano+ n’kuwalamula kuti: “Musamaope milungu ina.+ Musamaigwadire kapena kuitumikira kapenanso kupereka nsembe kwa iyo.+
2 Yehova wanena kuti: “Musaphunzire njira za anthu a mitundu ina ngakhale pang’ono,+ ndipo musamaope zizindikiro zakumwamba, chifukwa anthu a mitundu ina amachita mantha ndi zizindikirozo.+