Levitiko 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite+ zimene amachita anthu a ku Iguputo kumene munali kukhala, ndipo musakachite+ zimene amachita m’dziko la Kanani, kumene ndikukulowetsani. Musakatsatire mfundo zawo. Levitiko 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo musatsatire mfundo za mitundu imene ndikuichotsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+ Deuteronomo 12:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Samala kuti usagwidwe mumsampha wawo,+ pambuyo poti awonongedwa ndi kuchotsedwa pamaso pako, kutinso usafufuze za milungu yawo kuti, ‘Kodi mitundu imeneyi inali kutumikira bwanji milungu yawo? Ndithudi inenso ndidzachita zomwezo.’
3 Musachite+ zimene amachita anthu a ku Iguputo kumene munali kukhala, ndipo musakachite+ zimene amachita m’dziko la Kanani, kumene ndikukulowetsani. Musakatsatire mfundo zawo.
23 Ndipo musatsatire mfundo za mitundu imene ndikuichotsa pamaso panu,+ chifukwa iwo amachita zonsezi ndipo amandinyansa.+
30 Samala kuti usagwidwe mumsampha wawo,+ pambuyo poti awonongedwa ndi kuchotsedwa pamaso pako, kutinso usafufuze za milungu yawo kuti, ‘Kodi mitundu imeneyi inali kutumikira bwanji milungu yawo? Ndithudi inenso ndidzachita zomwezo.’