Salimo 106:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iwo anayamba kusakanikirana ndi mitundu ina,+Ndi kuyamba kuphunzira zochita zawo.+ Ezekieli 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndinawauza kuti, ‘Aliyense wa inu ataye zinthu zake zonyansa zimene amaziyang’anitsitsa pozilambira+ ndipo musadziipitse ndi mafano onyansa a ku Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+ Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+
7 Ine ndinawauza kuti, ‘Aliyense wa inu ataye zinthu zake zonyansa zimene amaziyang’anitsitsa pozilambira+ ndipo musadziipitse ndi mafano onyansa a ku Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+
4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+