Ekisodo 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ndamva kung’ung’udza kwa ana a Isiraeli.+ Auze kuti, ‘Madzulo kuli kachisisira* mudzadya nyama, ndipo m’mawa mudzadya mkate ndi kukhuta.+ Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+ Levitiko 11:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi. Levitiko 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Choncho mudzipatule monga anthu oyera,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.
12 “Ndamva kung’ung’udza kwa ana a Isiraeli.+ Auze kuti, ‘Madzulo kuli kachisisira* mudzadya nyama, ndipo m’mawa mudzadya mkate ndi kukhuta.+ Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+
44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.