Ezekieli 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ndinawauza kuti, ‘Aliyense wa inu ataye zinthu zonyansa zimene akuzitumikira. Musadziipitse ndi mafano onyansa* a ku Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+
7 Kenako ndinawauza kuti, ‘Aliyense wa inu ataye zinthu zonyansa zimene akuzitumikira. Musadziipitse ndi mafano onyansa* a ku Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+