Ezekieli 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Koma unayamba kudalira kukongola kwako+ ndipo unakhala hule chifukwa cha kutchuka kwa dzina lako.+ Unayamba kuchita uhule mosadziletsa ndi munthu aliyense wodutsa m’njira.+ Kukongola kwako unakupereka kwa anthu odutsawo.
15 “‘Koma unayamba kudalira kukongola kwako+ ndipo unakhala hule chifukwa cha kutchuka kwa dzina lako.+ Unayamba kuchita uhule mosadziletsa ndi munthu aliyense wodutsa m’njira.+ Kukongola kwako unakupereka kwa anthu odutsawo.