Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Solomo anayamba kutsatira Asitoreti,+ mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi Milikomu,+ chonyansa cha Aamoni.

  • Salimo 106:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iwo anayamba kusakanikirana ndi mitundu ina,+

      Ndi kuyamba kuphunzira zochita zawo.+

  • Yesaya 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Taonani! Mzinda wokhulupirika uja+ wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+ ndipo zachilungamo zinali kukhala mwa iye,+ koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+

  • Yesaya 57:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Unaika chizindikiro chachikumbutso chako kuseri kwa chitseko ndi kuseri kwa felemu.+ Iwe unavula n’kukwera mtunda kupita kumeneko uli kutali ndi ine. Unakulitsa bedi lako,+ ndipo unachita nawo pangano. Unkakonda kugona nawo pabedi+ ndipo unaona chiwalo cha mwamuna.

  • Yeremiya 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Ine ndinaphwanya goli lako kukhala zidutswazidutswa kalekale.+ Ndinadula zingwe zimene anakumanga nazo. Koma iwe unati: “Sindikutumikirani,” ndipo unagona motangadza+ paphiri lililonse lalitali ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira+ n’kumachita uhule+ pamenepo.

  • Hoseya 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulankhula kudzera mwa Hoseya, ndipo Yehova anauza Hoseya kuti: “Pita+ ukakwatire mkazi amene adzachita dama. Pamenepo udzakhala ndi ana chifukwa cha dama la mkazi wakoyo. Pakuti mwanjira yofanana ndi zimenezi, dzikoli latembenuka ndi kusiya kutsatira Yehova chifukwa cha dama.”+

  • Yakobo 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Achigololo+ inu, kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko n’kudziika pa udani ndi Mulungu?+ Choncho, aliyense amene akufuna kukhala bwenzi+ la dziko akudzisandutsa mdani wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena