Ezekieli 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi zambiri anthu amapatsa mahule mphatso,+ koma iweyo umapereka mphatso kwa zibwenzi zako zonse.+ Umawapatsa chiphuphu kuti abwere kwa iwe kuchokera kumalo onse ozungulira kuti adzachite nawe zauhule.+
33 Nthawi zambiri anthu amapatsa mahule mphatso,+ koma iweyo umapereka mphatso kwa zibwenzi zako zonse.+ Umawapatsa chiphuphu kuti abwere kwa iwe kuchokera kumalo onse ozungulira kuti adzachite nawe zauhule.+