12 Ndidzawononga mitengo yake ya mpesa+ ndi ya mkuyu+ imene iye anali kunena kuti: “Imeneyi ndi mphatso imene amuna ondikonda kwambiri anandipatsa.” Koma ine ndidzachititsa mitengoyo kukhala ngati nkhalango,+ ndipo zilombo zakutchire zidzaidya ndi kuiwononga.