1 Akorinto 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+
18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+