Genesis 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usakhale wopambana, chifukwa ndi khalidwe lako lotayirira ngati madzi osefukira,+ unakwera pogona bambo ako.+ Unaipitsa bedi langa pa nthawiyo.+ Anagonapo ndithu ameneyu! Miyambo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi akasupe ako amwazike panja,+ ndipo mitsinje yako yamadzi imwazike m’mabwalo a mumzinda? Miyambo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero pali chifukwa chanji choti usangalalire ndi mkazi wachilendo mwana wanga, kapena choti ukumbatirire chifuwa cha mkazi wina?+ Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+
4 Usakhale wopambana, chifukwa ndi khalidwe lako lotayirira ngati madzi osefukira,+ unakwera pogona bambo ako.+ Unaipitsa bedi langa pa nthawiyo.+ Anagonapo ndithu ameneyu!
20 Chotero pali chifukwa chanji choti usangalalire ndi mkazi wachilendo mwana wanga, kapena choti ukumbatirire chifuwa cha mkazi wina?+
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+