Deuteronomo 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Usabweretse malipiro+ a hule kapena malipiro a galu*+ m’nyumba ya Yehova Mulungu wako kuti ukwaniritse lonjezo lililonse, chifukwa zonsezo ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako. Ezekieli 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi zambiri anthu amapatsa mahule mphatso,+ koma iweyo umapereka mphatso kwa zibwenzi zako zonse.+ Umawapatsa chiphuphu kuti abwere kwa iwe kuchokera kumalo onse ozungulira kuti adzachite nawe zauhule.+ Luka 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma atangofika mwana wanuyu,+ amene anadya chuma chanu ndi mahule,+ mwamuphera mwana wa ng’ombe wamphongo wonenepa bwino.’+
18 Usabweretse malipiro+ a hule kapena malipiro a galu*+ m’nyumba ya Yehova Mulungu wako kuti ukwaniritse lonjezo lililonse, chifukwa zonsezo ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako.
33 Nthawi zambiri anthu amapatsa mahule mphatso,+ koma iweyo umapereka mphatso kwa zibwenzi zako zonse.+ Umawapatsa chiphuphu kuti abwere kwa iwe kuchokera kumalo onse ozungulira kuti adzachite nawe zauhule.+
30 Koma atangofika mwana wanuyu,+ amene anadya chuma chanu ndi mahule,+ mwamuphera mwana wa ng’ombe wamphongo wonenepa bwino.’+