Salimo 80:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 N’chifukwa chiyani mwagwetsa mpanda wake wamiyala?+Ndipo n’chifukwa chiyani anthu onse odutsa mumsewu akuthyola zipatso zake?+ Yesaya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano amuna inu, ndikuuzani zimene ndichite ndi munda wanga wa mpesa: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,+ ndipo ndiutentha.+ Ndigumula mpanda wake wamiyala ndipo mundawo udzangokhala malo oti azipondapondapo.+
12 N’chifukwa chiyani mwagwetsa mpanda wake wamiyala?+Ndipo n’chifukwa chiyani anthu onse odutsa mumsewu akuthyola zipatso zake?+
5 Tsopano amuna inu, ndikuuzani zimene ndichite ndi munda wanga wa mpesa: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,+ ndipo ndiutentha.+ Ndigumula mpanda wake wamiyala ndipo mundawo udzangokhala malo oti azipondapondapo.+