Yesaya 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Phazi lidzaupondaponda. Mapazi a munthu wosautsika ndi mapazi a anthu onyozeka, adzaupondaponda.”+ Maliro 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+
15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+