Salimo 89:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mwagwetsa makola ake onse amiyala.+Mizinda yake yamipanda yolimba mwaisandutsa mabwinja.+ Yesaya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano amuna inu, ndikuuzani zimene ndichite ndi munda wanga wa mpesa: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,+ ndipo ndiutentha.+ Ndigumula mpanda wake wamiyala ndipo mundawo udzangokhala malo oti azipondapondapo.+
5 Tsopano amuna inu, ndikuuzani zimene ndichite ndi munda wanga wa mpesa: Ndichotsa zomera zimene zinali ngati mpanda wa mundawo,+ ndipo ndiutentha.+ Ndigumula mpanda wake wamiyala ndipo mundawo udzangokhala malo oti azipondapondapo.+