2 Mbiri 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sisakiyo analanda mizinda ya Yuda+ yomwe inali ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo pamapeto pake anafika ku Yerusalemu.+ Yeremiya 52:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+ Maliro 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+
4 Sisakiyo analanda mizinda ya Yuda+ yomwe inali ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo pamapeto pake anafika ku Yerusalemu.+
14 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+
2 Yehova wameza malo okhala a Yakobo. Sanamvere chisoni malo ake alionse.+Mu ukali wake, iye wagwetsa mipanda yolimba kwambiri+ ya mwana wamkazi wa Yuda.Waipitsa ufumu+ ndi akalonga+ ake ndipo wawagwetsera pansi.+