Salimo 89:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Mwakana moipidwa pangano la mtumiki wanu.Mwanyoza chisoti chake chachifumu mwa kuchiponyera pansi.+ Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+ Ezekieli 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndidzawononga, ndidzawononga, ndidzawononga ufumu.*+ Ufumu umenewu sudzaperekedwa kwa wina aliyense kufikira atabwera amene ali woyenerera mwalamulo kuutenga,+ ndipo ndidzaupereka kwa iye.’+
39 Mwakana moipidwa pangano la mtumiki wanu.Mwanyoza chisoti chake chachifumu mwa kuchiponyera pansi.+
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
27 Ine ndidzawononga, ndidzawononga, ndidzawononga ufumu.*+ Ufumu umenewu sudzaperekedwa kwa wina aliyense kufikira atabwera amene ali woyenerera mwalamulo kuutenga,+ ndipo ndidzaupereka kwa iye.’+