Salimo 74:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo atentha malo anu opatulika.+Aipitsa ndi kugwetsera pansi chihema chokhala ndi dzina lanu.+ Maliro 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chisoti chathu chachifumu chagwa.+ Tsoka kwa ife chifukwa tachimwa!+ Ezekieli 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chotsa nduwira* ndipo vula chisoti chachifumu.+ Zinthu zasintha tsopano.+ Kweza munthu wotsika+ ndipo tsitsa munthu wokwezeka.+
26 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Chotsa nduwira* ndipo vula chisoti chachifumu.+ Zinthu zasintha tsopano.+ Kweza munthu wotsika+ ndipo tsitsa munthu wokwezeka.+