2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+ Yesaya 64:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nyumba yathu yoyera ndiponso yokongola+ imene makolo athu anali kukutamandiranimo,+ yasanduka chinthu chofunika kuchitentha pamoto,+ ndipo zinthu zathu zonse zabwinozabwino+ zasakazidwa.
9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+
11 Nyumba yathu yoyera ndiponso yokongola+ imene makolo athu anali kukutamandiranimo,+ yasanduka chinthu chofunika kuchitentha pamoto,+ ndipo zinthu zathu zonse zabwinozabwino+ zasakazidwa.