Yeremiya 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova wanena kuti, ‘Tsopano ndikulamula ndi kubweretsanso adaniwo kumzinda uno.+ Iwo adzamenyana ndi mzindawu ndipo adzaulanda ndi kuutentha.+ Pamenepo, mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa bwinja ndipo simudzapezeka munthu wokhalamo.’”+ Yeremiya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo Akasidi adzabweranso ndithu kudzamenyana ndi mzinda uno, kuulanda ndi kuutentha ndi moto.”+
22 “Yehova wanena kuti, ‘Tsopano ndikulamula ndi kubweretsanso adaniwo kumzinda uno.+ Iwo adzamenyana ndi mzindawu ndipo adzaulanda ndi kuutentha.+ Pamenepo, mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa bwinja ndipo simudzapezeka munthu wokhalamo.’”+