Yeremiya 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wanena kuti, ‘Ndidzapereka lamulo ndipo ndidzachititsa kuti adaniwo abwererenso mumzinda uno. Iwo adzamenyana ndi mzindawu ndipo adzaulanda nʼkuuwotcha ndi moto.+ Mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa bwinja ndipo simudzapezeka wokhalamo.’”+
22 Yehova wanena kuti, ‘Ndidzapereka lamulo ndipo ndidzachititsa kuti adaniwo abwererenso mumzinda uno. Iwo adzamenyana ndi mzindawu ndipo adzaulanda nʼkuuwotcha ndi moto.+ Mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa bwinja ndipo simudzapezeka wokhalamo.’”+