Yeremiya 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova wanena kuti, ‘Tsopano ndikulamula ndi kubweretsanso adaniwo kumzinda uno.+ Iwo adzamenyana ndi mzindawu ndipo adzaulanda ndi kuutentha.+ Pamenepo, mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa bwinja ndipo simudzapezeka munthu wokhalamo.’”+
22 “Yehova wanena kuti, ‘Tsopano ndikulamula ndi kubweretsanso adaniwo kumzinda uno.+ Iwo adzamenyana ndi mzindawu ndipo adzaulanda ndi kuutentha.+ Pamenepo, mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa bwinja ndipo simudzapezeka munthu wokhalamo.’”+