2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake. Yeremiya 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 M’chaka cha 9 cha ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 10,+ Nebukadirezara mfumu ya Babulo pamodzi ndi gulu lake lonse lankhondo anafika ku Yerusalemu ndi kuzungulira mzindawo.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
39 M’chaka cha 9 cha ulamuliro wa Zedekiya mfumu ya Yuda, m’mwezi wa 10,+ Nebukadirezara mfumu ya Babulo pamodzi ndi gulu lake lonse lankhondo anafika ku Yerusalemu ndi kuzungulira mzindawo.+