Genesis 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pambuyo pake Harana anamwalira mumzinda wa Akasidi+ wa Uri,+ kumene anabadwira. Anamwalira bambo ake Tera adakali ndi moyo. 2 Mafumu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri.
28 Pambuyo pake Harana anamwalira mumzinda wa Akasidi+ wa Uri,+ kumene anabadwira. Anamwalira bambo ake Tera adakali ndi moyo.
2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri.