2 Mafumu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri. Machitidwe 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo anasamuka m’dziko la Akasidi ndi kukakhala ku Harana. Kumeneko, pambuyo pa imfa ya bambo ake,+ Mulungu anamuuza kuti asamukire m’dziko lino limene inu mukukhala tsopano.+
2 Tsopano Yehova anayamba kum’tumizira Yehoyakimu magulu a achifwamba a Akasidi,+ a Asiriya, a Amowabu,+ ndi a ana a Amoni. Ankawatumiza ku Yuda kuti awononge dzikolo mogwirizana ndi mawu a Yehova+ amene analankhula kudzera mwa atumiki ake, aneneri.
4 Pamenepo anasamuka m’dziko la Akasidi ndi kukakhala ku Harana. Kumeneko, pambuyo pa imfa ya bambo ake,+ Mulungu anamuuza kuti asamukire m’dziko lino limene inu mukukhala tsopano.+