2 Mafumu 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zimenezi Elisa anamwalira ndipo anamuika m’manda.+ Tsopano panali magulu a achifwamba+ achimowabu+ amene ankabwera m’dzikolo kumayambiriro kwa chaka chilichonse.
20 Pambuyo pa zimenezi Elisa anamwalira ndipo anamuika m’manda.+ Tsopano panali magulu a achifwamba+ achimowabu+ amene ankabwera m’dzikolo kumayambiriro kwa chaka chilichonse.