Salimo 139:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati ndingakwere kumwamba, inu mudzakhala komweko.+Ndipo ngati ndingayale bedi langa ku Manda, taonani! inunso mudzakhala komweko.+
8 Ngati ndingakwere kumwamba, inu mudzakhala komweko.+Ndipo ngati ndingayale bedi langa ku Manda, taonani! inunso mudzakhala komweko.+