Yobu 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Manda ndi ovundukuka pamaso pake,+Ndipo malo a chiwonongeko n’ngosavundikira. Miyambo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+
11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+