Yobu 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Manda ndi ovundukuka pamaso pake,+Ndipo malo a chiwonongeko n’ngosavundikira. Salimo 139:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati ndingakwere kumwamba, inu mudzakhala komweko.+Ndipo ngati ndingayale bedi langa ku Manda, taonani! inunso mudzakhala komweko.+
8 Ngati ndingakwere kumwamba, inu mudzakhala komweko.+Ndipo ngati ndingayale bedi langa ku Manda, taonani! inunso mudzakhala komweko.+