2 Mbiri 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+ Yeremiya 52:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+
19 Iyo inatentha nyumba ya Mulungu woona+ ndi kugwetsa mpanda+ wa Yerusalemu. Ababulowo anatenthanso ndi moto nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri za mzindawo ndi zinthu zake zonse zabwinozabwino,+ mpaka zonse zinawonongedwa.+
13 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu ndi nyumba zonse za mu Yerusalemu.+ Anatenthanso nyumba iliyonse ya munthu wotchuka.+