Yeremiya 38:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Akazi anu onse ndi ana anu aamuna akutuluka nawo panja kupita nawo kwa Akasidi, ndipo inuyo simudzapulumuka m’manja mwa Akasidiwo,+ koma dzanja la mfumu ya Babulo lidzakugwirani. Mzinda uno adzautentha chifukwa cha inu.”+ Amosi 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzatumiza moto mu Yuda ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Yerusalemu.’+
23 “Akazi anu onse ndi ana anu aamuna akutuluka nawo panja kupita nawo kwa Akasidi, ndipo inuyo simudzapulumuka m’manja mwa Akasidiwo,+ koma dzanja la mfumu ya Babulo lidzakugwirani. Mzinda uno adzautentha chifukwa cha inu.”+