Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iwo anapha ana a Zedekiya iye akuona,+ kenako Zedekiyayo anam’chititsa khungu.+ Atatero anamumanga ndi maunyolo amkuwa+ n’kupita naye ku Babulo.+

  • 2 Mbiri 36:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kuwonjezera apo, Nebukadinezara anagwira anthu amene sanaphedwe ndi lupanga ndipo anawatenga kupita nawo ku Babulo.+ Anthuwo anakakhala antchito+ ake ndi a ana ake kufikira pamene ufumu wa Perisiya+ unayamba kulamulira.

  • Yeremiya 39:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zitatero mfumu ya Babulo inapha+ ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, Zedekiyayo akuona.+ Inaphanso akuluakulu onse a ku Yuda.+

  • Yeremiya 52:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linayamba kuthamangitsa mfumuyo+ ndipo Zedekiya anamupeza+ m’chipululu cha Yeriko. Zitatero gulu lonse lankhondo la Zedekiya linabalalika n’kumusiya yekha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena