2 Mafumu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo+ ku Ribila m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+ Salimo 137:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 137 Tinakhala pansi+ m’mphepete mwa mitsinje ya ku Babulo,+Ndipo tinalira titakumbukira Ziyoni.+
21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo+ ku Ribila m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+