Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndine amene ndikuuza madzi akuya kuti, ‘Iphwa ndipo mitsinje yako yonse ndidzaiumitsa.’+

  • Yeremiya 50:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+ ndipo anthu ake amachita zinthu mosaganiza chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.

  • Yeremiya 51:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Iwe mkazi wokhala pamadzi ambiri,+ wokhala ndi chuma chochuluka,+ mapeto ako afika ndipo nthawi yako+ yoti uzipanga phindu yatha.+

  • Yeremiya 51:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Akukanenanso kuti malo owolokera mtsinje alandidwa+ ndipo ngalawa zagumbwa* zatenthedwa. Amuna ankhondo nawonso asokonezeka.”+

  • Ezekieli 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 M’chaka cha 30, m’mwezi wachinayi, pa tsiku lachisanu la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka+ ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.+

  • Danieli 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndipo pa tsiku la 24 la mwezi woyamba, pamene ndinali m’mbali mwa mtsinje waukulu, mtsinje wa Hidekeli,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena