Yeremiya 50:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+Ndipo anthu ake amachita zinthu ngati amisala chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 50:38 Yeremiya, ptsa. 161-162 Ulosi wa Danieli, ptsa. 150-151 Mawu a Mulungu, ptsa. 123-125
38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+Ndipo anthu ake amachita zinthu ngati amisala chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.