-
Ezekieli 43:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Zimene ndinaonazo zinali zofanana ndi zimene ndinaona m’masomphenya ena.+ Zinali zofanana ndi masomphenya amene ndinaona pamene ndinapita kukawononga mzinda.*+ Ndinaona zinthu zofanana ndi zimene ndinaona m’mphepete mwa mtsinje wa Kebara.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.
-