-
Ezekieli 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndinayamba kuona masomphenya, ndipo ndinaona mphepo yamkuntho+ ikuchokera kumpoto. Ndinaonanso mtambo waukulu+ ndi moto walawilawi.+ Mtambowo unali wowala ndipo unali kuwalitsa malo onse ozungulira pamenepo. Pakati pa motowo panali powala ngati siliva wosakanikirana ndi golide, wooneka ngati akuchokera pakati pa motowo.+
-