Ezekieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova analankhula+ ndi Ezekieli,+ mwana wa wansembe Buzi, pamene anali m’dziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Dzanja la Yehova linafika pa iye kumeneko.+ Ezekieli 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero ndinanyamuka n’kupita kuchigwako. Kumeneko ndinangoona kuti ulemerero wa Yehova waimirira,+ ngati ulemerero umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+
3 Yehova analankhula+ ndi Ezekieli,+ mwana wa wansembe Buzi, pamene anali m’dziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Dzanja la Yehova linafika pa iye kumeneko.+
23 Chotero ndinanyamuka n’kupita kuchigwako. Kumeneko ndinangoona kuti ulemerero wa Yehova waimirira,+ ngati ulemerero umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara.+ Nditaona zimenezo, ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+