Ezekieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova analankhula ndi Ezekieli,* mwana wa wansembe Buzi, pamene anali mʼdziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Kumeneko mphamvu za Yehova zinayamba kugwira ntchito pa iye.*+
3 Yehova analankhula ndi Ezekieli,* mwana wa wansembe Buzi, pamene anali mʼdziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Kumeneko mphamvu za Yehova zinayamba kugwira ntchito pa iye.*+