Ezekieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’chaka cha 30, m’mwezi wachinayi, pa tsiku lachisanu la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka+ ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.+
1 M’chaka cha 30, m’mwezi wachinayi, pa tsiku lachisanu la mweziwo, pamene ndinali pakati pa anthu amene anali ku ukapolo+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara,+ kumwamba kunatseguka+ ndipo ndinayamba kuona masomphenya a Mulungu.+