2 Mafumu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu ya Babulo inatengera ku Babulo amuna onse olimba mtima okwana 7,000, amisiri ndi anthu omanga makoma achitetezo okwana 1,000, ndi amuna onse amphamvu omenya nkhondo.+ Yeremiya 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo ndidzakupereka m’manja mwa anthu ofunafuna moyo wako,+ m’manja mwa amene umawaopa, m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo ndiponso m’manja mwa Akasidi.+
16 Mfumu ya Babulo inatengera ku Babulo amuna onse olimba mtima okwana 7,000, amisiri ndi anthu omanga makoma achitetezo okwana 1,000, ndi amuna onse amphamvu omenya nkhondo.+
25 Ndipo ndidzakupereka m’manja mwa anthu ofunafuna moyo wako,+ m’manja mwa amene umawaopa, m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo ndiponso m’manja mwa Akasidi.+