Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chotero iye anatengera Yehoyakini+ ku Babulo.+ Anatenga ku Yerusalemu mayi a mfumuyo,+ akazi ake, nduna za panyumba yake,+ ndi akuluakulu a m’dzikolo, n’kuwapititsa ku Babulo.

  • Yeremiya 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Yehova wanena kuti: “Kenako Zedekiya mfumu ya Yuda, atumiki ake ndi anthu onse, onse opulumuka ku mliri, lupanga ndi njala yaikulu mumzinda uwu, ndidzawapereka m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo. Ndidzawapereka m’manja mwa adani awo ndi m’manja mwa amene akufuna moyo wawo. Nebukadirezara adzawapha ndi lupanga+ ndipo sadzawamvera chisoni, kuwakomera mtima kapena kuwachitira chifundo.”’+

  • Yeremiya 34:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Anthu amenewa ndidzawapereka m’manja mwa adani awo ndi m’manja mwa onse ofuna moyo wawo.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka m’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena