1 Mafumu 18:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+ 2 Mafumu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu inu, ndiitanireni woimba zeze.”+ Woimba zezeyo atangoyamba kuimba, dzanja+ la Yehova linakhala pa Elisa. Ezekieli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+
46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+
15 Anthu inu, ndiitanireni woimba zeze.”+ Woimba zezeyo atangoyamba kuimba, dzanja+ la Yehova linakhala pa Elisa.
14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+