46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+
3 Yehova analankhula+ ndi Ezekieli,+ mwana wa wansembe Buzi, pamene anali m’dziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Dzanja la Yehova linafika pa iye kumeneko.+
8M’chaka cha 6, m’mwezi wa 6, pa tsiku lachisanu la mweziwo, ndinali nditakhala m’nyumba mwanga ndipo akuluakulu a Yuda anali atakhala pamaso panga.+ Pamenepo, dzanja la Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, linafika pa ine.+